Yobu 26:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komatu zimenezi ndi kambali kakang’ono chabe ka zochita zake,+Ndipo timangomva kunong’ona kwapansipansi kwa mawu ake.Koma kodi mabingu ake amphamvu, angawamvetse ndani?”+ Miyambo 30:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inetu ndilibe nzeru,+ ndipo sindidziwa nzeru zimene zili ndi Woyera Koposa.+
14 Komatu zimenezi ndi kambali kakang’ono chabe ka zochita zake,+Ndipo timangomva kunong’ona kwapansipansi kwa mawu ake.Koma kodi mabingu ake amphamvu, angawamvetse ndani?”+