Genesis 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako Abulahamu anayamba kum’pempherera iye kwa Mulungu woona.+ Chotero Mulungu anachiritsa Abimeleki ndi mkazi wake, ndi akapolo ake aakazi, moti iwo anayamba kubereka ana. Yakobo 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pemphero lachikhulupiriro lidzachiritsa wodwalayo,+ ndipo Yehova adzamulimbitsa.+ Ndiponso ngati anachita machimo, adzakhululukidwa.+
17 Kenako Abulahamu anayamba kum’pempherera iye kwa Mulungu woona.+ Chotero Mulungu anachiritsa Abimeleki ndi mkazi wake, ndi akapolo ake aakazi, moti iwo anayamba kubereka ana.
15 Pemphero lachikhulupiriro lidzachiritsa wodwalayo,+ ndipo Yehova adzamulimbitsa.+ Ndiponso ngati anachita machimo, adzakhululukidwa.+