Genesis 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako, Abulahamu anamwalira ali wokalamba, atakhala ndi moyo wabwino, wautali ndi wokhutira, ndipo anaikidwa m’manda n’kugona ndi makolo ake.+
8 Kenako, Abulahamu anamwalira ali wokalamba, atakhala ndi moyo wabwino, wautali ndi wokhutira, ndipo anaikidwa m’manda n’kugona ndi makolo ake.+