Yobu 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Iwo amafufuzafufuza mu mdima+ mopanda kuwala,Kuti awachititse kuyendayenda ngati munthu woledzera.+ Miyambo 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Njira ya oipa ili ngati mdima.+ Iwo sadziwa chimene chimawapunthwitsa.+
25 Iwo amafufuzafufuza mu mdima+ mopanda kuwala,Kuti awachititse kuyendayenda ngati munthu woledzera.+