Salimo 35:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndinene ndi mtima wanga wonse kuti:+“Inu Yehova, ndani angafanane ndi inu,+Amene mumalanditsa wosautsika m’manja mwa munthu wamphamvu kuposa iyeyo,+Amene mumalanditsa wozunzika ndi wosauka m’manja mwa munthu amene akumulanda zinthu zake?”+
10 Ndinene ndi mtima wanga wonse kuti:+“Inu Yehova, ndani angafanane ndi inu,+Amene mumalanditsa wosautsika m’manja mwa munthu wamphamvu kuposa iyeyo,+Amene mumalanditsa wozunzika ndi wosauka m’manja mwa munthu amene akumulanda zinthu zake?”+