Yobu 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ana ake aamuna anali kuchita phwando+ kunyumba ya aliyense wa iwo, tsiku lina kwa wina, tsiku lina kwa wina, ndipo anali kuitana alongo awo atatu kuti adzadye ndi kumwera limodzi.
4 Ana ake aamuna anali kuchita phwando+ kunyumba ya aliyense wa iwo, tsiku lina kwa wina, tsiku lina kwa wina, ndipo anali kuitana alongo awo atatu kuti adzadye ndi kumwera limodzi.