Danieli 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Amaulula zinthu zozama ndi zinthu zobisika+ ndipo amadziwa zimene zili mu mdima.+ Komanso wazunguliridwa ndi kuwala.+ Mateyu 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Choncho musawaope, pakuti palibe chobisika chimene sichidzaululika, ndipo palibe chinsinsi chimene sichidzadziwika.+ 1 Akorinto 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chotero musaweruze+ kalikonse nthawi isanakwane, mpaka Ambuye adzafike.+ Akadzafika adzaunika zinsinsi za mu mdima+ ndi kuonetsa poyera+ zolingalira za m’mitima, ndipo aliyense adzatamandidwa yekha ndi Mulungu.+
22 Amaulula zinthu zozama ndi zinthu zobisika+ ndipo amadziwa zimene zili mu mdima.+ Komanso wazunguliridwa ndi kuwala.+
26 Choncho musawaope, pakuti palibe chobisika chimene sichidzaululika, ndipo palibe chinsinsi chimene sichidzadziwika.+
5 Chotero musaweruze+ kalikonse nthawi isanakwane, mpaka Ambuye adzafike.+ Akadzafika adzaunika zinsinsi za mu mdima+ ndi kuonetsa poyera+ zolingalira za m’mitima, ndipo aliyense adzatamandidwa yekha ndi Mulungu.+