Salimo 139:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndipo mdimawo sudzakhala mdima wandiweyani kwa inu,+Koma usiku udzakuwalirani ngati masana.+Mdima udzangokhala ngati kuwala.+ Aheberi 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino. Ndipotu ife tikuyenera kudzayankha pa zochita zathu kwa Mulungu amene amaona zonseyo.+
12 Ndipo mdimawo sudzakhala mdima wandiweyani kwa inu,+Koma usiku udzakuwalirani ngati masana.+Mdima udzangokhala ngati kuwala.+
13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino. Ndipotu ife tikuyenera kudzayankha pa zochita zathu kwa Mulungu amene amaona zonseyo.+