Salimo 25:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musakumbukire machimo a pa unyamata wanga ndi zolakwa zanga.+Ndikumbukireni malinga ndi kukoma mtima kwanu kosatha,+Ndiponso chifukwa cha ubwino wanu, inu Yehova.+ Yeremiya 31:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nditabwerera kwa inu ndinadzimvera chisoni.+ Mutandithandiza kuzindikira ndinadzimenya pantchafu chifukwa cha chisoni.+ Ndinachita manyazi ndipo ndinanyazitsidwa+ chifukwa cha chitonzo cha paubwana wanga.’”+
7 Musakumbukire machimo a pa unyamata wanga ndi zolakwa zanga.+Ndikumbukireni malinga ndi kukoma mtima kwanu kosatha,+Ndiponso chifukwa cha ubwino wanu, inu Yehova.+
19 Nditabwerera kwa inu ndinadzimvera chisoni.+ Mutandithandiza kuzindikira ndinadzimenya pantchafu chifukwa cha chisoni.+ Ndinachita manyazi ndipo ndinanyazitsidwa+ chifukwa cha chitonzo cha paubwana wanga.’”+