Yobu 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ngati ndachimwa, ndingakuchiteni chiyani Inu amene mumaonetsetsa anthu?+N’chifukwa chiyani mwalunjika ine, kuti ndikhale cholemetsa kwa inu?
20 Ngati ndachimwa, ndingakuchiteni chiyani Inu amene mumaonetsetsa anthu?+N’chifukwa chiyani mwalunjika ine, kuti ndikhale cholemetsa kwa inu?