Yakobo 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tamverani tsopano inu amene mumati: “Lero kapena mawa tipita kumzinda wakutiwakuti ndipo tikatha chaka kumeneko. Tikachita malonda kumeneko ndi kupeza phindu.”+
13 Tamverani tsopano inu amene mumati: “Lero kapena mawa tipita kumzinda wakutiwakuti ndipo tikatha chaka kumeneko. Tikachita malonda kumeneko ndi kupeza phindu.”+