Miyambo 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuwala kwa anthu olungama kudzawachititsa kusangalala.+ Koma nyale ya anthu oipa idzazimitsidwa.+ Miyambo 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 pakuti aliyense woipa alibe tsogolo,+ ndipo nyale ya anthu oipa idzazimitsidwa.+