Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 21:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Kodi nyale ya oipa imazimitsidwa kangati?+

      Ndipo tsoka lawo limawagwera kangati?

      Kodi ndi kangati pamene Mulungu amawakwiyira ndi kuwalanga?+

  • Salimo 73:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Pakuti onse okhala kutali ndi inu adzatheratu.+

      Mudzawononga ndithu aliyense wochita chigololo mwa kukusiyani.+

  • Miyambo 13:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kuwala kwa anthu olungama kudzawachititsa kusangalala.+ Koma nyale ya anthu oipa idzazimitsidwa.+

  • Miyambo 20:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Aliyense wotemberera bambo ake ndi mayi ake,+ nyale yake idzazimitsidwa kukagwa mdima.+

  • Mateyu 8:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 pamene ana a ufumuwo+ adzaponyedwa kunja kumdima. Kumeneko adzalira ndi kukukuta mano.”+

  • Yuda 13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ali ngatinso mafunde oopsa a panyanja otulutsa thovu la zinthu zoyenera kuwachititsa manyazi,+ ndiponso nyenyezi zosochera, zimene azisungira mdima wandiweyani wosatha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena