Salimo 42:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Odana nane akunditonza kwambiri moti zikungokhala ngati mafupa anga aphwanyidwa,+Pakuti anthu akundifunsa tsiku lonse kuti: “Mulungu wako ali kuti?”+
10 Odana nane akunditonza kwambiri moti zikungokhala ngati mafupa anga aphwanyidwa,+Pakuti anthu akundifunsa tsiku lonse kuti: “Mulungu wako ali kuti?”+