Salimo 73:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Inu Yehova, anthu amenewa ali ngati maloto amene aiwalika podzuka.+Choncho pamene mukuimirira mudzawakana mochititsa manyazi.+ Salimo 90:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwawawonongeratu,+ ndipo amangozimiririka ngati maloto.+M’mawa amakhala ngati msipu wobiriwira umene watsitsimuka.+
20 Inu Yehova, anthu amenewa ali ngati maloto amene aiwalika podzuka.+Choncho pamene mukuimirira mudzawakana mochititsa manyazi.+
5 Mwawawonongeratu,+ ndipo amangozimiririka ngati maloto.+M’mawa amakhala ngati msipu wobiriwira umene watsitsimuka.+