Agalatiya 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma Kefa+ atabwera ku Antiokeya,+ ndinamutsutsa pamasom’pamaso, chifukwa anali wolakwa.+