Salimo 33:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kumwamba kunalengedwa ndi mawu a Yehova,+Ndipo makamu ake onse analengedwa ndi mpweya wa m’kamwa mwake.+ Salimo 104:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mukatumiza mzimu wanu zimalengedwa.+Ndipo mumachititsa dziko kukhala latsopano.
6 Kumwamba kunalengedwa ndi mawu a Yehova,+Ndipo makamu ake onse analengedwa ndi mpweya wa m’kamwa mwake.+