Genesis 36:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yobabi atamwalira, Husamu wa kudziko la Atemani,+ anayamba kulamulira m’malo mwake.+ Yeremiya 49:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ponena za Edomu, Yehova wa makamu wanena kuti: “Kodi nzeru+ zinatha ku Temani?+ Kodi anthu ozindikira sakuperekanso malangizo anzeru? Kodi nzeru zawo zavunda?+
7 Ponena za Edomu, Yehova wa makamu wanena kuti: “Kodi nzeru+ zinatha ku Temani?+ Kodi anthu ozindikira sakuperekanso malangizo anzeru? Kodi nzeru zawo zavunda?+