Genesis 37:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ana ake onse aamuna ndi aakazi anali kupita kukam’tonthoza,+ koma iye anali kukana kutonthozedwa. Anali kunena kuti:+ “Ayi! Ndidzalira mpaka kutsikira ku Manda* kumene kuli mwana wanga.” Ndipo bambo akewo anapitiriza kumulira.
35 Ana ake onse aamuna ndi aakazi anali kupita kukam’tonthoza,+ koma iye anali kukana kutonthozedwa. Anali kunena kuti:+ “Ayi! Ndidzalira mpaka kutsikira ku Manda* kumene kuli mwana wanga.” Ndipo bambo akewo anapitiriza kumulira.