Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 39:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Mumtima mwanga munatentha moto.+

      Pamene ndinali kuusa moyo, moto unali kuyakabe.

      Choncho ndinati:

  • Yeremiya 20:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Choncho ndinanena kuti: “Sindidzanenanso za iye ndipo sindidzalankhulanso m’dzina lake.”+ Koma mumtima mwangamu, mawu ake anali ngati moto woyaka. Anali ngati moto woyaka umene autsekera m’mafupa anga. Choncho ndinatopa ndi kudziletsa kuti ndisalankhule moti sindinathenso kupirira.+

  • Machitidwe 18:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Mwamuna ameneyu analangizidwa njira ya Yehova ndi mawu a pakamwa. Ndiyeno popeza kuti anali wodzipereka kwambiri chifukwa chakuti anali ndi mzimu woyera,+ anali kulankhula ndi kuphunzitsa molondola za Yesu. Koma anali kudziwa za ubatizo+ wa Yohane wokha basi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena