Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 32:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Chifukwa ndili ndi mawu ambiri.

      Mzimu wandikanikiza+ m’mimba mwanga.

  • Salimo 39:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Mumtima mwanga munatentha moto.+

      Pamene ndinali kuusa moyo, moto unali kuyakabe.

      Choncho ndinati:

  • Yeremiya 6:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndadzazidwa ndi mkwiyo wa Yehova. Ndatopa ndi kukhala chete.”+

      “Tsanulira mkwiyowo pa mwana amene ali mumsewu+ ndipo nthawi yomweyo uutsanulirenso pa kagulu ka anyamata okondana. Mwamuna pamodzi ndi mkazi wake, munthu wachikulire pamodzi ndi munthu wokalamba, onsewo adzagwidwa.+

  • Amosi 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Mkango wabangula!+ Ndani sachita mantha? Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa walankhula! Ndani sanenera?’+

  • Machitidwe 4:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Koma ife sitingaleke kulankhula zinthu zimene tinaziona ndi kuzimva.”+

  • Machitidwe 18:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Tsopano Sila+ ndi Timoteyo+ atafika kuchokera ku Makedoniya, Paulo anatanganidwa kwambiri ndi ntchito yolalikira mawu a Mulungu. Iye anali kuchitira umboni kwa Ayuda ndi kuwatsimikizira kuti Yesu ndiyedi Khristu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena