Genesis 31:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma usiku m’maloto,+ Mulungu anafikira Labani Msiriyayo+ n’kumuuza kuti: “Samala kuti usanene chilichonse chosokoneza zochita za Yakobo.”+
24 Koma usiku m’maloto,+ Mulungu anafikira Labani Msiriyayo+ n’kumuuza kuti: “Samala kuti usanene chilichonse chosokoneza zochita za Yakobo.”+