Miyambo 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mwana wanga, usayende nawo limodzi panjira.+ Letsa phazi lako kuti lisayende panjira yawo.+ Miyambo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Usalowe panjira ya oipa,+ ndipo usalunjike kunjira ya ochita zoipa.+