Salimo 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Wodala+ ndi munthu amene sayenda motsatira malangizo a anthu oipa,+Saima m’njira ya anthu ochimwa,+Ndipo sakhala pansi pamodzi ndi anthu onyoza.+ 1 Akorinto 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Musasocheretsedwe. Kugwirizana ndi anthu oipa kumawononga makhalidwe abwino.+
1 Wodala+ ndi munthu amene sayenda motsatira malangizo a anthu oipa,+Saima m’njira ya anthu ochimwa,+Ndipo sakhala pansi pamodzi ndi anthu onyoza.+