Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 22:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ahaziya nayenso anayenda m’njira za anthu a m’nyumba ya Ahabu+ chifukwa amayi ake+ ndi amene anali kumulangiza kuti azichita zoipa.

  • Yobu 21:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Komatu, ulemerero wawo saupeza chifukwa cha mphamvu zawo.+

      Malangizo a anthu oipa atalikirana nane.+

  • Salimo 64:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Ndibiseni kuti ndisamve zinsinsi za anthu ochita zoipa,+

      Kuti ndisamve phokoso la anthu ochita zovulaza anzawo,+

  • Mateyu 26:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Iwo anali kupangana+ zoti agwire Yesu mochenjera ndi kumupha.

  • Machitidwe 9:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Tsopano patapita masiku ambiri, Ayudawo anasonkhana pamodzi ndi kupangana zoti amuphe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena