Salimo 56:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Amandiukira ndi kundibisalira,+Iwo nthawi zonse amaonetsetsa mmene ndikuyendera,+Pamene akundidikirira kuti awononge moyo wanga.+ Salimo 109:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu woipa ndiponso munthu wachinyengo andinenera zoipa ndi pakamwa pawo.+Iwo anena za ine ndi lilime lonama.+
6 Amandiukira ndi kundibisalira,+Iwo nthawi zonse amaonetsetsa mmene ndikuyendera,+Pamene akundidikirira kuti awononge moyo wanga.+
2 Munthu woipa ndiponso munthu wachinyengo andinenera zoipa ndi pakamwa pawo.+Iwo anena za ine ndi lilime lonama.+