Salimo 49:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Palibe ngakhale mmodzi wa iwo amene angathe kuwombola m’bale wake,+Kapena kumuperekera dipo* kwa Mulungu, Mlaliki 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Palibe munthu amene ali ndi mphamvu pa mzimu kuti auletse mzimuwo.+ Palibenso amene ali ndi mphamvu pa tsiku la imfa.+ Palibe amene samenya nawo nkhondo,+ ndipo kuchita zoipa sikudzapulumutsa amene amachita zoipawo.+
7 Palibe ngakhale mmodzi wa iwo amene angathe kuwombola m’bale wake,+Kapena kumuperekera dipo* kwa Mulungu, Mlaliki 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Palibe munthu amene ali ndi mphamvu pa mzimu kuti auletse mzimuwo.+ Palibenso amene ali ndi mphamvu pa tsiku la imfa.+ Palibe amene samenya nawo nkhondo,+ ndipo kuchita zoipa sikudzapulumutsa amene amachita zoipawo.+
8 Palibe munthu amene ali ndi mphamvu pa mzimu kuti auletse mzimuwo.+ Palibenso amene ali ndi mphamvu pa tsiku la imfa.+ Palibe amene samenya nawo nkhondo,+ ndipo kuchita zoipa sikudzapulumutsa amene amachita zoipawo.+