1 Samueli 25:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Patapita masiku 10, Yehova anakantha+ Nabala ndipo anafa. Danieli 2:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Munapitiriza kuchiyang’ana kufikira mwala unadulidwa kuphiri koma osati ndi manja a munthu.+ Mwalawo unamenya chifanizirocho kumapazi ake achitsulo chosakanizika ndi dongo ndipo unawapera.+
34 Munapitiriza kuchiyang’ana kufikira mwala unadulidwa kuphiri koma osati ndi manja a munthu.+ Mwalawo unamenya chifanizirocho kumapazi ake achitsulo chosakanizika ndi dongo ndipo unawapera.+