Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 2:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Zidzakhala choncho chifukwa munaona kuti mwala unadulidwa kuphiri koma osati ndi manja a munthu,+ ndipo unaphwanya chitsulo, mkuwa, dongo, siliva ndi golide.+ Inu mfumu, Mulungu Wamkulu+ wakudziwitsani zimene zidzachitike m’tsogolo.+ Maloto amenewa ndi odalirika ndipo kumasulira kwake ndi kokhulupirika.”+

  • Danieli 7:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kenako anamupatsa ulamuliro,+ ulemerero,+ ndi ufumu+ kuti anthu a mitundu yosiyanasiyana, olankhula zinenero zosiyanasiyana azimutumikira.+ Ulamuliro wake udzakhalapo mpaka kalekale ndipo sudzatha. Ufumu wake sudzawonongedwa.+

  • Danieli 7:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 “‘Ufumu, ulamuliro, ndi ulemerero wa maufumu a padziko lonse lapansi zinaperekedwa kwa oyera a Wamkulukulu.+ Ufumu wawo+ udzakhalapo mpaka kalekale ndipo maulamuliro onse adzawatumikira ndi kuwamvera.’+

  • Chivumbulutso 12:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mkaziyo anabereka mwana wamwamuna,+ mnyamata amene adzakusa mitundu yonse ndi ndodo yachitsulo.+ Ndipo mwana wakeyo anatengedwa msangamsanga n’kupititsidwa kwa Mulungu ndi kumpando wake wachifumu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena