Luka 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho iye ananena kuti: “Munthu wina wa m’banja lachifumu anapita kudziko lakutali kuti akalandire ufumu ndi kubwerako.+ Luka 22:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho ndikuchita nanu pangano,+ mmene Atate wanga wachitira pangano la ufumu ndi ine,+ Yohane 3:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Atate amakonda Mwana wake+ ndipo anapereka zinthu zonse m’manja mwake.+
12 Choncho iye ananena kuti: “Munthu wina wa m’banja lachifumu anapita kudziko lakutali kuti akalandire ufumu ndi kubwerako.+