Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 7:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 “‘Ufumu, ulamuliro, ndi ulemerero wa maufumu a padziko lonse lapansi zinaperekedwa kwa oyera a Wamkulukulu.+ Ufumu wawo+ udzakhalapo mpaka kalekale ndipo maulamuliro onse adzawatumikira ndi kuwamvera.’+

  • Luka 12:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 “Musaope,+ kagulu ka nkhosa+ inu, chifukwa Atate wanu wavomereza kukupatsani ufumu.+

  • 2 Timoteyo 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Tikapitiriza kupirira, tidzalamuliranso limodzi ndi iye monga mafumu.+ Tikamukana,+ iyenso adzatikana,

  • Aheberi 12:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Ndiye chifukwa chake, poona kuti tidzalandira ufumu umene sungagwedezeke,+ tiyeni tipitirize kulandira kukoma mtima kwakukulu, kuti kudzera m’kukoma mtima kwakukulu kumeneko, tichitire Mulungu utumiki wopatulika m’njira yovomerezeka, ndipo tiuchite moopa Mulungu komanso mwaulemu waukulu.+

  • Yakobo 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Tamverani abale anga okondedwa. Mulungu anasankha anthu amene ali osauka+ m’dzikoli kuti akhale olemera+ m’chikhulupiriro ndi olandira cholowa cha ufumu umene anaulonjeza kwa omukonda,+ sanatero kodi?

  • Chivumbulutso 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 n’kutipanga kukhala mafumu+ ndi ansembe+ kwa Mulungu wake ndi Atate wake, kwa iyeyo kukhale ulemerero ndi mphamvu kwamuyaya.+ Ame.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena