Yobu 34:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 ‘Yobu sadziwa zimene akunena,+Ndipo amanena mawu osonyeza kuti iye ndi wosazindikira.’ Yobu 38:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Kodi amene akuphimba malangizo angaNdi mawu ake opanda nzeruyu ndani?+