Yobu 35:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yobu akatsegula pakamwa pake amalankhula zopanda pake.Amachulukitsa mawu osonyeza kuti palibe chimene akudziwa.”+ Yobu 38:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Kodi amene akuphimba malangizo angaNdi mawu ake opanda nzeruyu ndani?+ Yobu 42:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu munati, ‘Kodi amene akuphimba malangizo anga mopanda nzeruyu ndani?’+Chotero ine ndinalankhula, koma sindinali kuzindikiraZinthu zodabwitsa kwambiri kwa ine, zimene sindikuzidziwa.+
16 Yobu akatsegula pakamwa pake amalankhula zopanda pake.Amachulukitsa mawu osonyeza kuti palibe chimene akudziwa.”+
3 Inu munati, ‘Kodi amene akuphimba malangizo anga mopanda nzeruyu ndani?’+Chotero ine ndinalankhula, koma sindinali kuzindikiraZinthu zodabwitsa kwambiri kwa ine, zimene sindikuzidziwa.+