Salimo 33:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Taonani! Diso la Yehova lili pa anthu amene amamuopa,+Amene amayembekezera kukoma mtima kwake kosatha,+ Salimo 34:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Maso a Yehova ali pa olungama,+Ndipo makutu ake amamva kufuula kwawo kopempha thandizo.+
18 Taonani! Diso la Yehova lili pa anthu amene amamuopa,+Amene amayembekezera kukoma mtima kwake kosatha,+ Salimo 34:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Maso a Yehova ali pa olungama,+Ndipo makutu ake amamva kufuula kwawo kopempha thandizo.+