Yobu 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti mivi ya Wamphamvuyonse yandilasa,+Ndipo ine ndikumwa poizoni wa miviyo.+Zoopsa zochokera kwa Mulungu zasonkhana kuti zilimbane nane.+ Maliro 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wakunga uta wake+ ndipo wandisandutsa chinthu cholasapo mivi+ yake.
4 Pakuti mivi ya Wamphamvuyonse yandilasa,+Ndipo ine ndikumwa poizoni wa miviyo.+Zoopsa zochokera kwa Mulungu zasonkhana kuti zilimbane nane.+