Rute 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 kodi mungawadikirirebe mpaka atakula? Kodi mungadzisungebe osakwatiwa powadikirira? Ayi ndithu ana anga, zimene zinakuchitikirani zimandiwawa kwambiri, pakuti dzanja la Yehova landiukira.”+ Salimo 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti dzanja lanu linali kundilemera usana ndi usiku.+Mphamvu zanga zinauma ngati madzi m’nyengo yotentha ya chilimwe.+ [Seʹlah.]
13 kodi mungawadikirirebe mpaka atakula? Kodi mungadzisungebe osakwatiwa powadikirira? Ayi ndithu ana anga, zimene zinakuchitikirani zimandiwawa kwambiri, pakuti dzanja la Yehova landiukira.”+
4 Pakuti dzanja lanu linali kundilemera usana ndi usiku.+Mphamvu zanga zinauma ngati madzi m’nyengo yotentha ya chilimwe.+ [Seʹlah.]