Yobu 30:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Khungu langa linakhala lakuda+ ndipo linayoyoka pathupi panga.Mafupa anga anatentha chifukwa chouma. Salimo 63:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Inu Mulungu, ndinu Mulungu wanga, ine ndikukufunafunani.+Moyo wanga ukulakalaka inu.+Thupi langa lalefuka chifukwa cholakalaka inuM’dziko louma ndi lopanda chonde, lopanda madzi.+ Salimo 102:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti masiku a moyo wanga atha ndi kuzimiririka ngati utsi,+Ndipo mafupa anga atentha kwambiri ngati ng’anjo.+
30 Khungu langa linakhala lakuda+ ndipo linayoyoka pathupi panga.Mafupa anga anatentha chifukwa chouma.
63 Inu Mulungu, ndinu Mulungu wanga, ine ndikukufunafunani.+Moyo wanga ukulakalaka inu.+Thupi langa lalefuka chifukwa cholakalaka inuM’dziko louma ndi lopanda chonde, lopanda madzi.+
3 Pakuti masiku a moyo wanga atha ndi kuzimiririka ngati utsi,+Ndipo mafupa anga atentha kwambiri ngati ng’anjo.+