Salimo 38:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ine ndakhala ngati munthu wogontha, sindikumvetsera,+Ndakhala ngati munthu wosalankhula, sindikutsegula pakamwa.+ Mateyu 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma pamene ansembe aakulu komanso akulu anali kumuneneza,+ iye sanayankhe chilichonse.+
13 Koma ine ndakhala ngati munthu wogontha, sindikumvetsera,+Ndakhala ngati munthu wosalankhula, sindikutsegula pakamwa.+