Salimo 39:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndinakhala chete osalankhula kanthu.+Ndinakhala phee osanena ngakhale zinthu zabwino,+Ndipo ndinanyalanyaza ululu wanga. Salimo 39:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndinakhala chete.+ Sindinatsegule pakamwa panga,+Pakuti inu munachitapo kanthu.+ Amosi 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho, munthu wozindikira adzakhala chete pa nthawi imeneyo chifukwa chakuti idzakhala nthawi yoopsa.+ 1 Petulo 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamene anali kunenedwa zachipongwe,+ sanabwezere zachipongwe.+ Pamene anali kuvutika,+ sanawopseze, koma anali kudzipereka kwa iye+ amene amaweruza molungama.
2 Ndinakhala chete osalankhula kanthu.+Ndinakhala phee osanena ngakhale zinthu zabwino,+Ndipo ndinanyalanyaza ululu wanga.
13 Choncho, munthu wozindikira adzakhala chete pa nthawi imeneyo chifukwa chakuti idzakhala nthawi yoopsa.+
23 Pamene anali kunenedwa zachipongwe,+ sanabwezere zachipongwe.+ Pamene anali kuvutika,+ sanawopseze, koma anali kudzipereka kwa iye+ amene amaweruza molungama.