Chivumbulutso 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nditayang’ana, ndinaona hatchi* yoyera.+ Wokwerapo+ wake ananyamula uta.+ Iye anapatsidwa chisoti chachifumu,+ ndi kupita kukagonjetsa adani ake+ ndipo anapambana pa nkhondo yolimbana nawo.+
2 Nditayang’ana, ndinaona hatchi* yoyera.+ Wokwerapo+ wake ananyamula uta.+ Iye anapatsidwa chisoti chachifumu,+ ndi kupita kukagonjetsa adani ake+ ndipo anapambana pa nkhondo yolimbana nawo.+