Yobu 33:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kum’bweza kuti asapite kudzenje,+Kuti aunikiridwe ndi kuwala kwa anthu amene ali moyo.+ Salimo 56:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti inu mwalanditsa moyo wanga ku imfa.+Inu mwateteza phazi langa kuti lisapunthwe,+Kuti ndiyendeyende pamaso pa Mulungu m’kuwala kumene kumaunikira anthu amoyo.+
13 Pakuti inu mwalanditsa moyo wanga ku imfa.+Inu mwateteza phazi langa kuti lisapunthwe,+Kuti ndiyendeyende pamaso pa Mulungu m’kuwala kumene kumaunikira anthu amoyo.+