Salimo 54:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti pali anthu achilendo amene andiukira,Ndipo pali olamulira ankhanza amene akufuna moyo wanga.+Sanaike Mulungu patsogolo pawo.+ [Seʹlah.]
3 Pakuti pali anthu achilendo amene andiukira,Ndipo pali olamulira ankhanza amene akufuna moyo wanga.+Sanaike Mulungu patsogolo pawo.+ [Seʹlah.]