Luka 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Koma taonani! Wondipereka+ ndili naye limodzi patebulo pompano.+ Luka 22:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Koma Yesu anamufunsa kuti: “Yudasi, kodi ukupereka Mwana wa munthu mwa kupsompsona?”+