Salimo 18:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Koma mudzachititsa adani anga kugonja* pamaso panga,+Anthu odana nane kwambiri, ndidzawakhalitsa chete.+ Salimo 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu ochita zoipa atandiyandikira kuti adye mnofu wanga,+Popeza kuti iwo ndi ondiukira komanso adani anga,+Anapunthwa ndi kugwa.+
40 Koma mudzachititsa adani anga kugonja* pamaso panga,+Anthu odana nane kwambiri, ndidzawakhalitsa chete.+
2 Anthu ochita zoipa atandiyandikira kuti adye mnofu wanga,+Popeza kuti iwo ndi ondiukira komanso adani anga,+Anapunthwa ndi kugwa.+