Miyambo 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma oipa adzachotsedwa padziko lapansi+ ndipo achinyengo adzazulidwamo.+ Miyambo 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu adzadya zipatso zabwino kuchokera pa zipatso za pakamwa pake.+ Koma moyo wa anthu ochita zachinyengo umalakalaka kuchita chiwawa.+
2 Munthu adzadya zipatso zabwino kuchokera pa zipatso za pakamwa pake.+ Koma moyo wa anthu ochita zachinyengo umalakalaka kuchita chiwawa.+