Miyambo 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Munthu amakhutitsidwa ndi zabwino kuchokera ku zipatso za pakamwa pake,+ ndipo zochita za manja a munthu, zidzabwerera kwa iye.+ Miyambo 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mimba ya munthu imakhuta zipatso za pakamwa pake.+ Iye amakhuta ngakhale zokolola za milomo yake.+
14 Munthu amakhutitsidwa ndi zabwino kuchokera ku zipatso za pakamwa pake,+ ndipo zochita za manja a munthu, zidzabwerera kwa iye.+
20 Mimba ya munthu imakhuta zipatso za pakamwa pake.+ Iye amakhuta ngakhale zokolola za milomo yake.+