Miyambo 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Munthu amakhutitsidwa ndi zabwino kuchokera ku zipatso za pakamwa pake,+ ndipo zochita za manja a munthu, zidzabwerera kwa iye.+ Miyambo 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munthu wosonyeza kuzindikira pa zinthu adzapeza zabwino,+ ndipo wodala ndi munthu amene amakhulupirira Yehova.+ Miyambo 16:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Munthu wakhama amadzigwirira yekha ntchito+ chifukwa chakuti pakamwa pake pamamukakamiza kwambiri.+
14 Munthu amakhutitsidwa ndi zabwino kuchokera ku zipatso za pakamwa pake,+ ndipo zochita za manja a munthu, zidzabwerera kwa iye.+
20 Munthu wosonyeza kuzindikira pa zinthu adzapeza zabwino,+ ndipo wodala ndi munthu amene amakhulupirira Yehova.+
26 Munthu wakhama amadzigwirira yekha ntchito+ chifukwa chakuti pakamwa pake pamamukakamiza kwambiri.+