Deuteronomo 31:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Tsopano dzilembereni nyimbo iyi+ ndi kuwaphunzitsa ana a Isiraeli.+ Muiike m’kamwa mwawo kuti nyimbo imeneyi ikhale mboni yanga pamaso pa ana a Isiraeliwo.+ 2 Samueli 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye ananenanso kuti, ana a Yuda+ aphunzitsidwe nyimboyi, yotchedwa “Uta.”+ Nyimbo imeneyi inalembedwa m’buku la Yasari:+
19 “Tsopano dzilembereni nyimbo iyi+ ndi kuwaphunzitsa ana a Isiraeli.+ Muiike m’kamwa mwawo kuti nyimbo imeneyi ikhale mboni yanga pamaso pa ana a Isiraeliwo.+
18 Iye ananenanso kuti, ana a Yuda+ aphunzitsidwe nyimboyi, yotchedwa “Uta.”+ Nyimbo imeneyi inalembedwa m’buku la Yasari:+