Yesaya 30:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pa chifukwa chimenechi, kwa inu cholakwa chanuchi chidzakhala ngati mpanda wautali kwambiri umene wang’aluka penapake n’kupendekeka,+ umene ukhoza kugwa mwadzidzidzi, mosayembekezereka.+
13 Pa chifukwa chimenechi, kwa inu cholakwa chanuchi chidzakhala ngati mpanda wautali kwambiri umene wang’aluka penapake n’kupendekeka,+ umene ukhoza kugwa mwadzidzidzi, mosayembekezereka.+