Salimo 62:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi mudzayesayesa kufikira liti kuti muphe munthu amene mumadana naye?+Nonsenu muli ngati khoma lopendekeka, khoma lamiyala limene akulikankha kuti ligwe.+ Luka 6:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Koma amene akumva ndi kusachita,+ ali ngati munthu womanga nyumba yopanda maziko padothi. Apanso mtsinje unasefukira n’kuwomba nyumbayo, ndipo nthawi yomweyo inagwa, mwakuti kugwa+ kwa nyumba imeneyo kunali kwamkokomo.”+
3 Kodi mudzayesayesa kufikira liti kuti muphe munthu amene mumadana naye?+Nonsenu muli ngati khoma lopendekeka, khoma lamiyala limene akulikankha kuti ligwe.+
49 Koma amene akumva ndi kusachita,+ ali ngati munthu womanga nyumba yopanda maziko padothi. Apanso mtsinje unasefukira n’kuwomba nyumbayo, ndipo nthawi yomweyo inagwa, mwakuti kugwa+ kwa nyumba imeneyo kunali kwamkokomo.”+